Librería Samer Atenea
Kálamo Books
Librería Elías (Asturias)
Librería Kolima (Madrid)
Librería Proteo (Málaga)
Fajar lives in the city and her dream is to visit her grandparents who live in the village for sometime. Fajar loves her grandparents and they love her too. She loves helping them in their daily work and listening to their stories. To make her dream come true, her parents take Fajar and her sibling to see their grandparents. Let us follow Fajar and see why she enjoys visiting her grandparents. Fajar amakhala mumzinda ndipo amalakalaka kukachezera agogo ake, omwe amakhala kumudzi. Fajar amakonda agogo ake, ndipo nawonso amamukonda. Kuti akwaniritse chikhumbo chake, makolo ake amapita naye limodzi ndi mchimwene wake kukachezera agogo awo. Tiyeni tipite ndi Fajar kuti tione chifukwa chake amasangalala kukachezera agogo ake.