Librería Samer Atenea
Librería Aciertas (Toledo)
Kálamo Books
Librería Perelló (Valencia)
Librería Elías (Asturias)
Donde los libros
Librería Kolima (Madrid)
Librería Proteo (Málaga)
Thandizani ana anu kukhala odzidalira powerenga okha Baibulo Aloreni kuwerenga okha nkhani zosangalatsa zosiyanasiyana za m’baibulo pa nthawi imene akufuna kutero. Mwakutero, adzakhala ndi lusa lomvetsa zinthu pawokha mwachangu ndi kuzigwilitsa bwino ntchito chomwe ndi chuma chokhazikika. Lolani kuti, chikondi cha Mulungu chomwe ndi chopanda malire, chiwalire pa miyoyo ya ana anu.